Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa cover

Podcast

Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa

Thru the Bible Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu …

Episodes

0
Indexing this feed

Episodes will appear here as soon as the worker finishes.

Prefer another app? Listen on Apple Podcasts